1 Mbiri 2:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Azichemwali awo anali Zeruya ndi Abigayeli.+ Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu+ ndi Asaheli.+ 17 Abigayeli anabereka Amasa+ ndipo bambo ake a Amasa anali Yeteri mbadwa ya Isimaeli.
16 Azichemwali awo anali Zeruya ndi Abigayeli.+ Zeruya anali ndi ana atatu: Abisai,+ Yowabu+ ndi Asaheli.+ 17 Abigayeli anabereka Amasa+ ndipo bambo ake a Amasa anali Yeteri mbadwa ya Isimaeli.