Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mbiri 2:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ndikutumiza munthu waluso ndi womvetsa zinthu, dzina lake Hiramu-abi.+ 14 Mayi ake ndi a fuko la Dani, koma bambo ake anali a ku Turo. Iye ndi wodziwa ntchito za golide, siliva, kopa, chitsulo, miyala, matabwa, ubweya wapepo, nsalu zabwino kwambiri komanso ulusi wabuluu ndi wofiira.+ Amathanso kujambula ndi kulemba mochita kugoba ndipo amadziwa kupanga chilichonse chimene angauzidwe.+ Iye azidzagwira ntchito limodzi ndi anthu anu aluso ndiponso anthu aluso a mbuye wanga Davide bambo anu.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani