-
Yesaya 64:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Poona zinthu zonsezi, kodi mupitiriza kumangokhala osachitapo kanthu, inu Yehova?
Kodi mungokhala chete nʼkumaonerera ife tikusautsidwa koopsa?+
-
-
Maliro 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Iye wathetsa mphamvu zonse za* Isiraeli atakwiya kwambiri.
-