Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 68:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake. Yesaya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake.
5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+