Salimo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Adani anga onse amandinyoza,+Makamaka anthu oyandikana nawo. Ndipo anthu ondidziwa amachita nane mantha.Akandiona ndili panja amandithawa.+ Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzapitiriza kunyoza mpaka liti?+ Kodi mdani adzachitira mwano dzina lanu mpaka kalekale?+ Salimo 79:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
11 Adani anga onse amandinyoza,+Makamaka anthu oyandikana nawo. Ndipo anthu ondidziwa amachita nane mantha.Akandiona ndili panja amandithawa.+
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzapitiriza kunyoza mpaka liti?+ Kodi mdani adzachitira mwano dzina lanu mpaka kalekale?+