-
Yesaya 49:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:
“Taona! Ineyo ndidzakwezera dzanja langa mitundu ya anthu,
Ndipo anthu a mitundu ina ndidzawakwezera chizindikiro.+
-