Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Nehemiya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako ndinayankha mfumuyo kuti: “Mfumu mukhale ndi moyo wautali! Ndilekerenji kuoneka wachisoni pamene mzinda umene makolo anga anaikidwako uli bwinja ndipo mageti ake anatenthedwa ndi moto?”+

  • Salimo 84:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Salimo 102:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndithudi inu mudzanyamuka nʼkusonyeza Ziyoni chifundo,+

      Chifukwa imeneyi ndi nthawi yoti mumusonyeze kukoma mtima kwanu.+

      Nthawi yoikidwiratu yakwana.+

      14 Atumiki anu amasangalala ndi miyala ya mpanda wake,+

      Ndipo amakonda ngakhale fumbi lake.+

  • Yesaya 62:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala chete,+

      Ndipo chifukwa cha Yerusalemu sindidzakhala phee

      Mpaka kulungama kwake kutawala kwambiri,+

      Ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+

  • Yeremiya 51:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Inu amene mwathawa lupanga, pitirizani kuthawa, musaime.+

      Kumbukirani Yehova pamene muli kutali kwambiri,

      Ndipo muziganizira Yerusalemu mumtima mwanu.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani