Salimo 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+ Nʼchifukwa chiyani mwanditaya? Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?+
2 Inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+ Nʼchifukwa chiyani mwanditaya? Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?+