Salimo 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandiiwala?+ Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?”+
9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandiiwala?+ Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?”+