2 Mafumu 25:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yeremiya 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Akasidi amene akumenyana ndi anthu amumzindawu adzabwera nʼkuyatsa mzindawu moti udzapseratu.+ Adzawotchanso nyumba zimene pamadenga ake anthu ankaperekerapo nsembe kwa Baala komanso nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.’+ Yeremiya 39:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Akasidi anawotcha nyumba ya mfumu ndi nyumba za anthu+ ndipo anagwetsa mpanda wa Yerusalemu.+
29 Akasidi amene akumenyana ndi anthu amumzindawu adzabwera nʼkuyatsa mzindawu moti udzapseratu.+ Adzawotchanso nyumba zimene pamadenga ake anthu ankaperekerapo nsembe kwa Baala komanso nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.’+
8 Kenako Akasidi anawotcha nyumba ya mfumu ndi nyumba za anthu+ ndipo anagwetsa mpanda wa Yerusalemu.+