Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+Wosangalala adzakhala amene adzakubwezereZimene iwe watichitira.+ Yeremiya 51:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Wowononga adzafikira Babulo.+Asilikali ake adzagwidwa,+Mauta awo adzathyoledwa,Chifukwa Yehova ndi Mulungu amene amapereka chilango choyenera.+ Iye adzabwezera ndithu.+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+Wosangalala adzakhala amene adzakubwezereZimene iwe watichitira.+
56 Wowononga adzafikira Babulo.+Asilikali ake adzagwidwa,+Mauta awo adzathyoledwa,Chifukwa Yehova ndi Mulungu amene amapereka chilango choyenera.+ Iye adzabwezera ndithu.+