Magazini Yophunzira
JANUARY 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 27 MPAKA APRIL 2, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
CHILE
Ofalitsa a kum’mwera kwa dziko la Chile akuyenda mphepete mwa mtsinje kudutsa m’nkhalango za m’mapiri a Andes. Akufuna kulalikira kwa anthu ochuluka pa nthawi imene sikukuzizira kwambiri.
OFALITSA
76,296
MAPHUNZIRO A BAIBULO
64,178
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
174,761
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.