Magazini Yophunzira
MARCH 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA MAY 1 MPAKA 28, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
ROMANIA
Mkulu wina ndi mkazi wake akulalikira aneba awo amene akukonza ubweya wa nkhosa. Iwo amaona kuti Lamlungu akaweruka kumisonkhano imakhala nthawi yabwino yofufuza anthu amene ali ngati nkhosa, kumpoto kwa Romania.
KULI OFALITSA
40,575
MAPHUNZIRO A BAIBULO
25,623
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
78,300
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.