Magazini Yophunzira
JULY 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: AUGUST 28–SEPTEMBER 24, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
POLAND
M’bale akuuza munthu uthenga wa m’Baibulo m’munda wa maapozi ku Grójec.
KULI OFALITSA
119,932
MAPHUNZIRO A BAIBULO
50,479
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
190,613
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.