Magazini Yophunzira
AUGUST 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: SEPTEMBER 25–OCTOBER 22, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
NETHERLANDS
Apainiya awiri ku Amsterdam akulalikira munthu amene akumana naye
KULI OFALITSA
29,839
MAPHUNZIRO A BAIBULO
12,802
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
51,404
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.