Magazini Yophunzira
NOVEMBER 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 25, 2017–JANUARY 28, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
NICARAGUA
Alongo awiri akulalikira munthu wamalonda m’tauni ya Tipitapa
KULI OFALITSA
28,642
MAPHUNZIRO A BAIBULO
42,298
OPEZEKA PACHIKUMBUTSO (2016)
88,308
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.