Magazini Yophunzira
December 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JANUARY 29–FEBRUARY 25, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
CÔTE D’IVOIRE
M’dziko la Côte d’Ivoire (lomwe kale linkatchedwa Ivory Coast) mumalimidwa koko wambiri yemwe amagwiritsidwa ntchito popanga chokoleti. Kokoyo amayamba amuyanika padzuwa. Mpainiya akusonyeza mlimi mitu imene ili m’kabuku kakuti Uthenga Wabwino
KULI OFALITSA
11,133
MAPHUNZIRO A BAIBULO
28,274
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
76,526
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.