Magazini Yophunzira
March 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: APRIL 30–JUNE 3, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
CROATIA
Abale awiri ali pamlatho wapafupi ndi nyumba imene inamangidwa m’ma 1500 pafupi ndi mzinda wa Split ndipo akupereka kapepala kwa munthu wogwira ntchito yopaka penti
OFALITSA
5,335
MAPHUNZIRO A BAIBULO
2,123
OPEZEKA PACHIKUMBUTSO (2016)
8,434
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.