September 11-17
Ezekieli 46-48
Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Aisiraeli Omwe Anachoka ku Ukapolo Analandira Madalitso”: (10 min.)
Ezek. 47:1, 7-12—M’dziko lobwezeretsedwalo anthu anali ndi zokolola zambiri (w99 3/1 10 ¶11-12)
Ezek. 47:13, 14—Banja lililonse linalandira cholowa chake (w99 3/1 10 ¶10)
Ezek. 48:9, 10—Malo asanagawidwe kwa anthu, anaika padera gawo lina la malowo monga “chopereka” kwa Yehova
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Ezek. 47:1, 8; 48:30, 32-34—N’chifukwa chiyani Ayuda amene anachokera ku ukapolo sankafunika kuona kukwaniritsidwa kwa mbali iliyonse ya masomphenya a Ezekieli onena za kachisi? (w99 3/1 11 ¶14)
Ezek. 47:6—N’chifukwa chiyani Ezekieli akutchulidwa kuti ndi “mwana wa munthu”? (it-2 1001)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 48:13-22
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp17.5 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp17.5—Sonyezani mmene mungapangire ulendo wobwereza pogwiritsa ntchito magazini imene munamusiyira pa ulendo woyamba. Kenako musonyezeni limodzi mwa mabuku amene timagwiritsa ntchito pophunzira Baibulo.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 35 ¶17—Muitanireni kumisonkhano.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (8 min.) Mukhoza kukambirana zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb17 64-65)
Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 6 ¶16-24, komanso tsamba 67
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 11 ndi Pemphero