Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.09 3
  • September 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.09 3

September 10-16

YOHANE 3-4

  • Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesu Analalikira Mayi Wachisamariya”: (10 min.)

    • Yoh. 4:6, 7​—Ngakhale kuti anali atatopa, Yesu anayamba kulankhula ndi mayi wachisamariya (“atatopa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 4:6, nwtsty)

    • Yoh. 4:21-24​—Zimene Yesu anachitazi zinachititsa kuti anthu ambiri amve uthenga wabwino

    • Yoh. 4:39-41​—Chifukwa cha khama limene Yesu anachita, Asamariya ambiri anayamba kumukhulupirira

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 3:29​—Kodi vesi limeneli likutanthauza chiyani? (“mnzake wa mkwati” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 3:29, nwtsty)

    • Yoh. 4:10​—Kodi n’kutheka kuti mayi wachisamariyayu ankaganiza chiyani pamene Yesu ananena za “madzi amoyo,” koma kodi Yesu ankatanthauza chiyani kwenikweni? (“madzi amoyo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 4:10, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 4:1-15

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsirani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) wp16.2 9 ¶2-5​—Mutu: Kodi Lemba la Yohane 4:23 Limatanthauza Chiyani?.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 77

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Mmene Mungayambire Kucheza ndi Anthu Kuti Muwalalikire Mwamwayi”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pomaliza limbikitsani onse kuti ayesetse kuyamba kucheza ndi munthu n’cholinga choti amulalikire. Ndiyeno pamsonkhano wotsatira wa mkati mwa mlungu, ofalitsa adzafotokoze zosangalatsa zimene zinachitika.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 4

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani