Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.10 2
  • Yesu Amasamalira Nkhosa Zake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesu Amasamalira Nkhosa Zake
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.10 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 9-10

Yesu Amasamalira Nkhosa Zake

10:1-5, 11, 14, 16

Yesu yemwe ndi m’busa wabwino, amadziwa bwino nkhosa zake. Amadziwa zomwe timafuna, zimene timachita bwino komanso zimene timalephera. Nazonso nkhosa zimadziwa bwino m’busa wawo komanso zimamudalira akamazitsogolera.

Kodi Yesu amakhala bwanji m’busa wabwino pankhani . . .

  • yosonkhanitsa nkhosa zake?

  • yotsogolera nkhosa zake?

  • yoteteza nkhosa zake?

  • yodyetsa nkhosa zake?

M’busa akulondera khola la nkhosa

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimayamikira zimene Yesu amachita pondisamalira?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani