October Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 2018 Zimene Tinganene October 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 9-10 Yesu Amasamalira Nkhosa Zake October 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 11-12 Muzitsanzira Yesu pa Nkhani Yochitira Ena Chifundo October 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 13-14 “Ndakupatsani Chitsanzo” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Chikondi—Musamakhale ndi Mtima Wofuna Kuchita Zofuna Zanu Zokha Komanso Musamakwiye October 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 15-17 “Simuli Mbali ya Dzikoli” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Chikondi—Muziteteza Mgwirizano Wathu Wamtengo Wapatali October 29–November 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 18-19 Yesu Anachitira Umboni Choonadi MOYO WATHU WACHIKHRISTU Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Chikondi—Muzisangalala ndi Choonadi