Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.10 3
  • October 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.10 3

October 14-20

1 Petulo 1-2

  • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalani Oyera”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Petulo.]

    • 1 Pet. 1:14, 15​—Khalidwe lathu komanso zomwe timaganiza ziyenera kukhala zoyera (w17.02 9 ¶5)

    • 1 Pet. 1:16​—Tiziyesetsa kutsanzira Mulungu wathu, amene ndi woyera (lvs 77 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • 1 Pet. 1:10-12​—Kodi tingakhale bwanji akhama mofanana ndi aneneri komanso angelo? (w08 11/15 21 ¶10)

    • 1 Pet. 2:25​—Kodi woyang’anira wathu wamkulu ndi ndani? (it-2 565 ¶3)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Pet. 1:3-9 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo.(th phunziro 3)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mugawireni chilichonse cha zinthu zomwe timagwiritsa ntchito pophunzitsa.(th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 28

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Uzikhala Waukhondo: (6 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako itanani ana omwe munawasankhiratu kuti abwere kutsogolo ndipo muwafunse mafunso otsatirawa: Kodi Mulungu anaika bwanji chilichonse pamalo ake? N’chiyani chimathandiza kuti mvuwu zikhale zaukhondo? N’chifukwa chiyani muyenera kumakonza kuchipinda kwanu?

  • “Yehova Amakonda Anthu Aukhondo”: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Mulungu Amakonda Anthu Aukhondo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 11:10-17

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani