October Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya Mboni za Yehova yophunzirira m’mwezi wa October 2019. Zimene Tinganene October 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YAKOBO 3-5 Muzisonyeza Nzeru Yochokera kwa Mulungu October 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 PETULO 1-2 “Khalani Oyera” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Amakonda Anthu Aukhondo October 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 PETULO 3-5 “Mapeto a Zinthu Zonse Ayandikira” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Munthu Akhoza Kusintha Akaona Ulemu Komanso Khalidwe Lanu Labwino October 28–November 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 PETULO 1-3 ‘Muzikumbukira Kukhalapo kwa Tsiku la Yehova’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mumakonda Kwambiri Mawu a Mulungu?