October 28–November 3
2 Petulo 1-3
Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikumbukira Kukhalapo kwa Tsiku la Yehova”: (10 min.)
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Petulo.]
2 Pet. 3:9, 10—Tsiku la Yehova lidzafika pa nthawi yake (w06 12/15 27 ¶11)
2 Pet. 3:11, 12—Tiyenera kuganizira kuti ndife anthu otani (w06 12/15 19 ¶18)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
2 Pet. 1:19—Kodi “nthanda” ikuimira ndani ndipo inatuluka liti, nanga tikudziwa bwanji kuti zimenezi zinachitika kale? (w08 11/15 22 ¶2)
2 Pet. 2:4—Kodi “Tatalasi” n’chiyani, ndipo angelo opanduka anaponyedwamo liti? (w08 11/15 22 ¶3)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Pet. 1:1-8 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 7)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 154-155 ¶3-4 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kodi Mumakonda Kwambiri Mawu a Mulungu? (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ankalemekeza Kwambiri Baibulo (William Tyndale).
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 12:1-8
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 64 ndi Pemphero