Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.11 6
  • November 25–December 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 25–December 1
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.11 6

November 25–December 1

CHIVUMBULUTSO 4-6

  • Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anthu 4 Okwera Pamahatchi”: (10 min.)

    • Chiv. 6:2​—Wokwera pahatchi yoyera ‘anapita kukagonjetsa’ (wp17.3 4 ¶3, 5)

    • Chiv. 6:4-6​—Pambuyo pake panabwera wokwera pahatchi yofiira ndi wokwera pahatchi yakuda (wp17.3 5 ¶2, 4-5)

    • Chiv. 6:8​—Kenako panabwera wokwera pahatchi yotuwa, yemwe Manda ankamutsatira (wp17.3 5 ¶8-10)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Chiv. 4:4, 6​—Kodi akulu 24 ndi zamoyo 4 zimaimira chiyani? (re 76-77 ¶8; 80 ¶19)

    • Chiv. 5:5​—N’chifukwa chiyani Yesu amatchedwa “Mkango wa fuko la Yuda”? (cf 36 ¶5-6)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 4:4-11 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 4)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) lvs 53 ¶15 (th phunziro 2)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 46

  • “Yehova Amakonda Munthu Wopereka Mokondwera”: (15 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu. Yambani ndi kuonera vidiyo yakuti Mmene Mungaperekere Zopereka pa Zipangizo za Makono. Uzani ofalitsa kuti akhoza kudziwa mmene angaperekere zopereka zawo akadina pamene alemba kuti Donations pa jw.org komanso pa JW Library kapena afufuze pa intaneti polemba mawu akuti donate.jw.org. Werengani kalata yochokera ku ofesi ya nthambi yoyamikira zopereka zomwe munapereka chaka chautumiki chapitachi. Yamikirani abale ndi alongo chifukwa chopereka mowolowa manja.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 13:9-14

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani