Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.11 6
  • Anthu 4 Okwera Pamahatchi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anthu 4 Okwera Pamahatchi
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.11 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 4-6

Anthu 4 Okwera Pamahatchi

6:2, 4-6, 8

Yesu wakwera hatchi yoyera ndipo akukoka uta; pambuyo pake pakubwera hatchi yofiira, yakuda komanso yotuwa

Yesu ‘anapita kukagonjetsa adani ake’ pamene anamenya nkhondo yolimbana ndi Satana komanso ziwanda zake n’kuwagwetsera padziko lapansi. Iye akupitirizabe kugonjetsa adani ake pothandiza komanso kuteteza atumiki ake m’masiku otsiriza ano. Komabe adzamaliza ntchito yolimbana ndi adaniwo akadzagonjetsa okwera pamahatchi atatu enawo. Iye adzachita zimenezi pankhondo ya Aramagedo ndipo kenako adzakonza zonse zomwe okwera pamahatchi atatu aja anawononga.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani