Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.01
  • “Anachitadi Momwemo”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Anachitadi Momwemo”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • “Anayenda Ndi Mulungu Woona”
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Kodi Nkhani ya Nowa Komanso Chigumula Ndi Nthano Chabe?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Chingalawa cha Nowa
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Chigumula Chisanachitike, Kodi Ndani Anamvera Mulungu Ndipo Ndani Amene Sanamumvere?
    Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.01
Nowa ndi mwana wake akumanga chingalawa, mwanayo wakwera pamakwerero a katawala ndipo akupaka phula chingalawacho.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 6-8

“Anachitadi Momwemo”

6:9, 13-16, 22

Taganizirani ntchito imene Nowa ndi banja lake anali nayo kuti amange chingalawa popanda zipangizo komanso njira zamakono zomangira.

  • Chingalawacho chinali chachikulu kwambiri. Chinali cha mamita 133 m’litali, mamita 22 m’lifupi komanso mamita 13 kupita m’mwamba

  • Ankafunika kugwetsa mitengo, kuidula, kenako n’kuipititsa kumene ankagwirira ntchito

  • Ankafunika kupaka phula mkati komanso kunja kwa chingalawacho

  • Ankafunikanso kusunga chakudya cha chaka chathunthu cha iyeyo ndi banja lake komanso zinyama

  • Ntchitoyi iyenera kuti inatenga zaka 40 kapena 50 kuti ithe

Kodi nkhaniyi ingatithandize bwanji ngati timaona kuti n’zovuta kuchita zimene Yehova amatiuza?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani