Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.11
  • November 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 9-15
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.11

NOVEMBER 9-15

LEVITIKO 1-3

  • Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chifukwa Chake Nsembe Zinkaperekedwa”: (10 min.)

    • [Onerani Vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Levitiko.]

    • Le 1:3; 2:1, 12​—Chifukwa chake nsembe zopsereza komanso zambewu zinkaperekedwa (it-2 525; 528 ¶4)

    • Le 3:1​—Chifukwa chake nsembe zachiyanjano zinkaperekedwa (it-2 526 ¶1)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 2:13​—N’chifukwa chiyani ankayenera kuperekanso mchere popereka nsembe iliyonse? (Eze 43:24; w04 5/15 22 ¶2)

    • Le 3:17​—N’chifukwa chiyani Aisiraeli sankaloledwa kudya mafuta, nanga tikuphunzirapo chiyani? (it-1 813; w04 5/15 22 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 1:6-17 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani Yokambirana. Onerani vidiyoyi koma muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime ndipo funsani omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 53

  • “‘Timakobidi Tiwiri Tating’ono’ Tamtengo Wapatali”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti ‘Muzipereka Mphatso kwa Yehova’. Werengani kalata yochokera kunthambi yothokoza zopereka zimene yalandira m’chaka cha utumiki chapitachi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) ia 11:12-20

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani