Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.11
  • November 30–December 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 30–December 6
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.11

NOVEMBER 30–DECEMBER 6

LEVITIKO 8-9

  • Nyimbo Na. 16 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Umboni Wakuti Yehova Ankawadalitsa”: (10 min.)

    • Le 8:6-9, 12​—Mose analonga anthu unsembe (it-1 1207)

    • Le 9:1-5​—Mtundu wonse wa Aisiraeli unkaona pamene ansembe ankapereka nsembe zanyama zoyambirira (it-1 1208 ¶8)

    • Le 9:23, 24​—Yehova anasonyeza kuti anavomereza ansembewo (w19.11 23 ¶13)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 8:6​—Kodi tingaphunzire chiyani pa lamulo lakuti ansembe a ku Isiraeli ankafunika kukhala aukhondo? (w14 11/15 9 ¶6)

    • Le 8:14-17​—Pamene ankakhazikitsa unsembe, n’chifukwa chiyani Mose ndi amene anapereka nsembe osati Aroni? (it-2 437 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 9:1-7 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako tchulani mfundo inayake yam’magazini yogawira ya Nsanja ya Olonda Na. 2 2020, ndipo perekani magaziniyo. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako musonyezeni webusaiti yathu ya jw.org n’kumupatsa khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 4)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 84 ¶6-7 (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 58

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Kulalikira Pogwiritsa Ntchito Foni”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Onerani ndi kukambirana vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) ia 12:18-25

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani