Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.11
  • Nsembe Yosonyeza Kuyamikira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nsembe Yosonyeza Kuyamikira
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Tizisonyeza Kuti Ndife Oyamikira
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Zimene Tingaphunzire M’buku la Levitiko
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • “Musamade Nkhawa ndi Kanthu Kalikonse”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.11
Banja la Chiisiraeli likudya nyama yoperekedwa monga nsembe yachiyanjano.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 6-7

Nsembe Yosonyeza Kuyamikira

7:11-15, 20

Nsembe zachiyanjano zimene Aisiraeli ankapereka zimatikumbutsa kufunika koyamikira Yehova kudzera m’mapemphero komanso m’makhalidwe athu.​—Afi 4:6, 7; Akl 3:15.

  • Tikamapemphera, kodi tingathokoze Yehova chifukwa cha zinthu ziti?​—1At 5:17, 18

  • Kodi kusonyeza kuti ndife oyamikira kumatithandiza bwanji?

  • Kodi munthu angamadye bwanji “patebulo la ziwanda,” nanga zimenezi zingasonyeze bwanji kuti munthuyo sayamikira Yehova?​—1Ak 10:20, 21

Mkazi wa Chiisiraeli akuyang’ana kumwamba ndipo akuthokoza Yehova.
    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani