Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.01 10-14
  • February 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 1-7
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.01 10-14

February 1-7

LEVITIKO 26-​27

  • Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mungatani Kuti Yehova Azikudalitsani?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 26:16​—Kodi tinganene kuti Yehova analanga bwanji Aisiraeli ndi matenda? (it-2 617)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 26:​18-​26 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)

  • Nkhani: (5 min.) w09 8/1 30​—Mutu: Kodi Mulungu Amafuna Kuti Ndizipereka Ndalama Zingati? (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 40

  • “Sankhani Kutumikira Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Zimene Munthu Angachite Kuti Abatizidwe.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 15:20-26 ndi Mfundo Zobwereza

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani