Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.03 12
  • March 29–April 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 29–April 4
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.03 12

March 29–April 4

NUMERI 15-16

  • Nyimbo Na. 101 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Samalani Kuti Musakhale Wonyada Ndi Wodzidalira”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 15:32-35​—Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhani imeneyi? (w98 9/1 20 ¶1-2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 15:8-16 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Ulendo Woyamba: Yesu​—Mt 16:16. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Nkhani: (5 min.) w15 5/15 15 ¶5-6​—Mutu: Kodi Kunyadira N’kosiyana Bwanji ndi Kunyada? (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 124

  • “Musamatsanzire Anthu Amene Ndi Osakhulupirika”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Musamatsanzire Anthu Osakhulupirika.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 18:9-17

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani