March Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, March-April 2021 March 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli March 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amatsogolera Anthu Ake March 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupewa Mtima Wodandaula? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mukukonzekera Chikumbutso? March 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Chikhulupiriro Chimatithandizira Kukhala Olimba Mtima KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri Mu Utumiki—Muzifunsa Mafunso March 29–April 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Samalani Kuti Musakhale Wonyada Ndi Wodzidalira MOYO WATHU WACHIKHRISTU Musamatsanzire Anthu Amene Ndi Osakhulupirika April 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Ine Ndine . . . Cholowa Chako” April 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muziyesetsa Kukhalabe Ofatsa Mukapanikizika April 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Amasintha Chizunzo N’kukhala Mwayi Wolalikira April 26–May 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzisankha Anzanu Mwanzeru KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene