February 7-13
1 SAMUELI 1-2
Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzimuuza Yehova Zamumtima Mwanu Mukamapemphera”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 2:10—N’chifukwa chiyani Hana anapemphera kuti Yehova ‘adzapereke mphamvu kwa mfumu yake’ pamene mu Isiraeli munalibe mfumu? (w05 3/15 21 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 1:1-18 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako m’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo kambiranani naye mwachidule kamutu kakuti “Zimene Mungachite Kuti Muzipindula Pophunzira Baibulo.” (th phunziro 20)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 03 mfundo 5 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Achinyamata, Muzicheza Momasuka ndi Makolo Anu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Moyo Wanga Wachinyamata—Kodi Ndingatani Kuti Ndizilankhulana Bwino ndi Makolo Anga?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 11:1-9
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero