January Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, January-February 2022 January 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kupereka Mnzako kwa Mdani N’koipa Kwambiri January 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kusamvera Malamulo a Mulungu Kumabweretsa Mavuto January 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzifunsira Nzeru kwa Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Chilengedwe Chimatithandiza Kuti Tizidalira Kwambiri Nzeru za Yehova January 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzisonyeza Chikondi Chokhulupirika MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Amatisonyeza Chikondi Chokhulupirika January 31–February 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzikhala ndi Makhalidwe Abwino KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muzithandiza Ophunzira Baibulo Anu Kuti Azipezeka Pamisonkhano February 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzimuuza Yehova Zamumtima Mwanu Mukamapemphera MOYO WATHU WACHIKHRISTU Achinyamata, Muzicheza Momasuka ndi Makolo Anu February 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amatiganizira MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zimene Tingaphunzire kwa Samueli February 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mfumu Yanu ndi Ndani? February 28–March 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Sauli Anali Wodzichepetsa Poyamba KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muzithandiza Ophunzira Baibulo Kuti Asamacheze ndi Anthu Olakwika KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene