CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Muzikhala ndi Makhalidwe Abwino
Rute ankachita zinthu moganizira ena (Ru 3:10; ia 5:18)
Rute ankadziwika kuti anali “mkazi wabwino kwambiri” (Ru 3:11; ia 5:21)
Yehova anaona makhalidwe abwino amene Rute anali nawo ndipo anamudalitsa (Ru 4:11-13; ia 5:25)
Lembani makhalidwe abwino amene mungakonde kuti muzidziwika nawo.