January 31–February 6
RUTE 3-4
Nyimbo Na. 39 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikhala ndi Makhalidwe Abwino”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Ru 4:6—Kodi munthu wowombola ‘akanawononga’ bwanji cholowa chake powombola mkazi? (w05 3/1 29 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ru 4:7-22 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzithandiza Ophunzira Baibulo Anu Kuti Azipezeka Pamisonkhano”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Azipezeka Pamisonkhano.
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 03 mfundo 4 (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 10:19-24, Kubweleza
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero