February 14-20
1 SAMUELI 3-5
Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amatiganizira”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 3:3—Kodi tikudziwa bwanji kuti Samueli sanagone m’Malo Oyera Koposa? (w05 3/15 21 ¶6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 3:1-18 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pa phunziro 01. (th phunziro 15)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 03 mfundo 6 (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Zimene Tingaphunzire kwa Samueli”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Zimene Tingaphunzire Kuchokera kwa Samueli.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 11:10-17
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero