Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.05 2
  • May 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 2-8
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.05 2

May 2-8

1 SAMUELI 27-29

  • Nyimbo Na. 71 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 28:15​—Kodi pamenepa Sauli “anaona” ndani? (w10 1/1 20 ¶4-5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 27:1-9 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Kuvutika​—Yak 1:13. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, komanso yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 129

  • Anakhalabe Olimba Pozunzidwa: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi tikuphunzira chiyani pa chitsanzo cha abale athu a ku Germany mu ulamuliro wa Nazi? Kodi tikuphunzira chiyani pa chitsanzo cha abale athu a ku Russia komanso dziko lomwe kale linali Soviet Union?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 14:13-19, Kubweleza

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani