May Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, May-June 2022 May 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo May 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu May 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Tikuphunzira Chiyani Kuchokera pa Nyimbo Yotchedwa “Uta”? MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Chikondi . . . Sichikondwera ndi Zosalungama” MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Chikondi . . . Chimayembekezera Zinthu Zonse” May 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzikhala Ndi Mantha Oyenera Poopa Kukhumudwitsa Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mwakonzeka Kukumana Ndi Zachiwawa? May 30–June 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Anachita Pangano ndi Davide MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzigwiritsa Ntchito Zimene Zikuchitika M’dera Lanu Mukakhala mu Utumiki June 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Davide Anasonyeza Chikondi Chokhulupirika June 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Musalole Kuti Zilakolako Zoipa Zizikulamulirani MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzidziletsa June 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzigwiritsa Ntchito Buku Lakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale Polimbitsa Chikhulupiriro Chanu mwa Yehova Ndi Yesu June 27–July 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Abisalomu Anaukira Chifukwa cha Kunyada MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Chikondi . . . Sichidzikuza” KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene