January 9-15
2 MAFUMU 24-25
Nyimbo Na. 60 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 24:3, 4—Kodi mavesiwa akutiphunzitsa chiyani zokhudza Yehova? (w05-CN 8/1 12:1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 24:1-6 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Pemphero—1Yo 5:14. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 15)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza, kenako yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 24
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero