Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.07 11
  • July 31–August 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 31–August 6
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.07 11

July 31–August 6

NEHEMIYA 3-4

  • Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ne 4:17, 18​—Kodi munthu angagwire bwanji ntchito yomanga ndi dzanja limodzi? (w06-CN 2/1 9:1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 3:15-24 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Kambiranani tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo m’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)

  • Nkhani: (5 min.) Km-CN 11/12​—Mutu: Muzisangalala Chifukwa Chogwira Ntchito Mwakhama. (th phunziro 10)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 91

  • Kugwira Ntchito ndi a Mboni za Yehova: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera kuti, Mogwirizana ndi zomwe mwaona muvidiyoyi, kodi khalidwe lathu pa malo ogwirira ntchito lingathandize bwanji anthu kukhala ndi maganizo oyenera okhudza a Mboni?

  • Zofunika Pampingo: (7 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 46

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 51 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani