Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.07 12
  • Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzikhalabe Wosangalala Ngakhale Pamene Zinthu Sizikuyenda Bwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.07 12
Amuna ndi akazi a Chiisiraeli akugwira mwakhama ntchito yomanganso mpanda wa Yerusalemu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?

Mkulu wa ansembe ndi abale ake sanadzione kukhala anthu apamwamba kwambiri ndipo anagwira nawo ntchito yomanganso mpanda wa Yerusalemu (Ne 3:1)

Anthu ena otchuka “sanagonjere” kuti agwire nawo ntchitoyo (Ne 3:5; w06-CN 2/1 10:1)

Akazi okhulupirika anagwira nawo ntchitoyi yomwe inali yovuta komanso yofuna mphamvu zambiri (Ne 3:12; w19.10 41:11)

Ntchito zambiri zimene zimachitika pampingo, zimafuna mphamvu kapena zimakhala zonyozeka komanso zina ena sangatione tikuzigwira.​—w04-CN 8/1 18:16.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimamva bwanji ndikamagwira ntchito zoterezi, zomwe zimathandiza pa ntchito ya uthenga wabwino?’​—1Ak 9:23.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani