Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.09 19
  • Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Anthu 12 Anapita Kukaona Dziko la Kanani
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mawu Omaliza Amene Yoswa Analimbikitsa Nawo Mtundu wa Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzidzichepetsa​—Muzipewa Kudzitama
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.09 19

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse

Kalebe anayamba kutumikira Yehova ali wachinyamata (Yos 14:7, 8)

Patapita nthawi, Kalebe anadalira Yehova kuti akwanitse utumiki wovuta womwe anamupatsa (Yos 14:10-12; w04 12/1 11:11)

Kalebe analandira madalitso chifukwa chotumikira Yehova ndi mtima wonse (Yos 14:13, 14; w06 10/1 18:11)

Zithunzi: Chithunzi cha mlongo wokhulupirika amene akupirira mavuto obwera chifukwa cha uchikulire. 1. Wakhala pansi atagwira ndodo ndipo akupemphera. 2. Akulalikira pa malo opezeka anthu ambiri ali ndi mlongo wachitsikana. 3. Akuonetsa zithunzi ana akumpingo kwawo. 4. Akumwetulira.

Chikhulupiriro cha Kalebe chinalimba chifukwa chotsatira malangizo a Yehova komanso kuona madalitso amene ankalandira. Ifenso tikamaona Yehova akuyankha mapemphero athu komanso kutitsogolera m’njira zosiyanasiyana zimatilimbikitsa kupitirizabe kum’tumikira.​—1Yo 5:14, 15.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani