Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.09 4
  • September 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.09 4

September 11-17

ESITERE 3-5

  • Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Est 4:​12-16—Kodi timamenyera bwanji ufulu wolambira ngati mmene Esitere ndi Moredekai anachitira? (kr 160:14)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Est 3:​1-9 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Ufumu—Mt 14:​19, 20. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 16)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 12 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 15)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 65

  • Khalani Bwenzi la Yehova—Nditsanzire Esitere: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka funsani ana omwe munawasankhiratu funso ili: Kodi mungatsanzire bwanji kulimba mtima kwa Esitere?

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff 49:6, Komanso zomwe taphunzira, kubwereza ndi zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani