GENESIS
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Mulungu anapuma pa tsiku la 7 (1-3)
Yehova Mulungu anapanga kumwamba ndi dziko lapansi (4)
Mwamuna ndi mkazi mʼmunda wa Edeni (5-25)
Munthu anapangidwa kuchokera kudothi (7)
Mtengo woletsedwa wodziwitsa chabwino ndi choipa (15-17)
Kulengedwa kwa mkazi (18-25)
3
4
5
6
Ana a Mulungu anakwatira akazi padziko lapansi (1-3)
Kubadwa kwa Anefili (4)
Yehova anamva chisoni chifukwa cha kuipa kwa anthu (5-8)
Nowa anapatsidwa ntchito yopanga chingalawa (9-16)
Mulungu ananena kuti adzabweretsa chigumula (17-22)
7
8
Kuphwa kwa madzi a chigumula (1-14)
Kutuluka mʼchingalawa (15-19)
Lonjezo la Mulungu lokhudza dziko lapansi (20-22)
9
Malangizo opita kwa anthu onse (1-7)
Pangano la utawaleza (8-17)
Maulosi okhudza mbadwa za Nowa (18-29)
10
Mitundu ya anthu (1-32)
Mbadwa za Yafeti (2-5)
Mbadwa za Hamu (6-20)
Mbadwa za Semu (21-31)
11
12
13
Abulamu anabwerera ku Kanani (1-4)
Abulamu anasiyana ndi Loti (5-13)
Mulungu anabwereza lonjezo lake kwa Abulamu (14-18)
14
15
16
17
Abulahamu adzakhala tate wa mitundu yambiri (1-8)
Pangano la mdulidwe (9-14)
Dzina la Sarai linasinthidwa kukhala Sara (15-17)
Analonjezedwa za kubadwa kwa Isaki (18-27)
18
Angelo atatu anapita kwa Abulahamu (1-8)
Analonjeza kuti Sara adzabereka mwana wamwamuna; Sara anaseka (9-15)
Abulahamu anapempha zokhudza Sodomu (16-33)
19
Angelo anapita kwa Loti (1-11)
Loti ndi banja lake anauzidwa kuti asamuke (12-22)
Kuwonongedwa kwa Sodomu ndi Gomora (23-29)
Loti ndi ana ake aakazi (30-38)
20
21
Kubadwa kwa Isaki (1-7)
Isimaeli ankaseka Isaki (8, 9)
Hagara ndi Isimaeli anathamangitsidwa (10-21)
Pangano la Abulahamu ndi Abimeleki (22-34)
22
23
24
25
Abulahamu anakwatiranso (1-6)
Imfa ya Abulahamu (7-11)
Ana a Isimaeli (12-18)
Kubadwa kwa Yakobo ndi Esau (19-26)
Esau anagulitsa ukulu wake (27-34)
26
Isaki ndi Rabeka ku Gerari (1-11)
Kukanganirana zitsime (12-25)
Pangano la Isaki ndi Abimeleki (26-33)
Akazi awiri a Chihiti a Esau (34, 35)
27
Yakobo anadalitsidwa ndi Isaki (1-29)
Esau ankafuna madalitso koma sanalape (30-40)
Esau anayamba kudana ndi Yakobo (41-46)
28
29
Yakobo anakumana ndi Rakele (1-14)
Yakobo anakonda Rakele (15-20)
Yakobo anakwatira Leya ndi Rakele (21-29)
Ana 4 aamuna a Yakobo amene Leya anamuberekera: Rubeni, Simiyoni, Levi ndi Yuda (30-35)
30
Biliha anabereka Dani ndi Nafitali (1-8)
Zilipa anabereka Gadi ndi Aseri (9-13)
Leya anabereka Isakara ndi Zebuloni (14-21)
Rakele anabereka Yosefe (22-24)
Ziweto za Yakobo zinachuluka (25-43)
31
Yakobo anachoka ku Kanani mozemba (1-18)
Labani anapezana ndi Yakobo (19-35)
Pangano la Yakobo ndi Labani (36-55)
32
Angelo anakumana ndi Yakobo (1, 2)
Yakobo anakonzekera kukumana ndi Esau (3-23)
Yakobo analimbana ndi mngelo (24-32)
33
34
35
Yakobo anachotsa milungu yachilendo (1-4)
Yakobo anabwerera ku Beteli (5-15)
Kubadwa kwa Benjamini; imfa ya Rakele (16-20)
Ana 12 a Isiraeli (21-26)
Imfa ya Isaki (27-29)
36
37
38
39
Yosefe mʼnyumba ya Potifara (1-6)
Yosefe anakana kugona ndi mkazi wa Potifara (7-20)
Yosefe anaikidwa mʼndende (21-23)
40
41
Yosefe anamasulira maloto a Farao (1-36)
Yosefe anapatsidwa udindo ndi Farao (37-46a)
Yosefe ankayangʼanira ntchito yogawa chakudya (46b-57)
42
Azichimwene ake a Yosefe anapita ku Iguputo (1-4)
Yosefe anakumana ndi azichimwene ake ndipo anawayesa (5-25)
Azichimwene ake a Yosefe anabwerera kwa Yakobo (26-38)
43
Ulendo wachiwiri wa azichimwene ake a Yosefe wopita ku Iguputo limodzi ndi Benjamini (1-14)
Yosefe anakumananso ndi azichimwene ake (15-23)
Phwando la Yosefe ndi azichimwene ake (24-34)
44
45
46
Yakobo ndi banja lake anasamukira ku Iguputo (1-7)
Mayina a anthu amene anasamukira ku Iguputo (8-27)
Yosefe anakumana ndi Yakobo ku Goseni (28-34)
47
Yakobo anakumana ndi Farao (1-12)
Yosefe anagwira ntchito yoyangʼanira mwanzeru (13-26)
Isiraeli anakhazikika ku Goseni (27-31)
48
49
50
Yosefe anaika mʼmanda Yakobo ku Kanani (1-14)
Yosefe anatsimikizira abale ake kuti anawakhululukira (15-21)
Masiku akumapeto kwa moyo wa Yosefe ndi imfa yake (22-26)