YESAYA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Bambo ndi ana ake opanduka (1-9)
Yehova amadana ndi kumulambira mwamwambo (10-17)
“Tiyeni tikambirane” (18-20)
Ziyoni adzabwezeretsedwa kukhala mzinda wokhulupirika (21-31)
2
3
4
5
Nyimbo yonena za munda wa mpesa wa Yehova (1-7)
Masoka amene anagwera munda wa mpesa wa Yehova (8-24)
Mulungu anakwiyira anthu ake (25-30)
6
Masomphenya okhudza Yehova ali mʼkachisi wake (1-4)
Milomo ya Yesaya inayeretsedwa (5-7)
Yesaya anapatsidwa utumiki (8-10)
“Mpaka liti, inu Yehova?” (11-13)
7
Uthenga wopita kwa Mfumu Ahazi (1-9)
Chizindikiro cha Emanueli (10-17)
Mavuto obwera chifukwa cha kusakhulupirika (18-25)
8
Kuukiridwa ndi Asuri (1-8)
Musachite mantha—“Mulungu ali nafe” (9-17)
Yesaya ndi ana ake anali ngati zizindikiro (18)
Muzifufuza chilamulo, osati kufunsira kwa ziwanda (19-22)
9
10
Dzanja la Mulungu lidzaukira Isiraeli (1-4)
Asuri—Ndodo yosonyezera mkwiyo wa Mulungu (5-11)
Kulangidwa kwa Asuri (12-19)
Otsala a Yakobo adzabwerera (20-27)
Mulungu adzaweruza Asuri (28-34)
11
12
13
14
Isiraeli adzakhala mʼdziko lake (1, 2)
Kunyozedwa kwa mfumu ya Babulo (3-23)
Dzanja la Yehova lidzaphwanya Asuri (24-27)
Uthenga wokhudza Filisitiya (28-32)
15
16
17
18
19
20
21
22
23
24
25
26
27
28
Tsoka kwa zidakwa za ku Efuraimu (1-6)
Ansembe ndi aneneri a ku Yuda akuyenda modzandira (7-13)
“Pangano ndi Imfa” (14-22)
Chitsanzo chosonyeza kuti malangizo a Yehova ndi anzeru (23-29)
29
30
Thandizo lochokera ku Iguputo ndi losathandiza ngakhale pangʼono (1-7)
Anthu anakana uthenga waulosi (8-14)
Mudzakhala amphamvu mukamadalira Mulungu (15-17)
Yehova amakomera mtima anthu ake (18-26)
Yehova adzapereka chilango kwa Asuri (27-33)
31
32
Mfumu ndi akalonga adzalamulira mwachilungamo chenicheni (1-8)
Chenjezo kwa akazi ochita zinthu motayirira (9-14)
Adzadalitsidwa akadzalandira mzimu (15-20)
33
34
35
36
37
Hezekiya anapempha thandizo kwa Mulungu kudzera mwa Yesaya (1-7)
Senakeribu anaopseza Yerusalemu (8-13)
Pemphero la Hezekiya (14-20)
Yesaya anapereka yankho lochokera kwa Mulungu (21-35)
Mngelo anapha Asuri 185,000 (36-38)
38
39
40
41
Amene adzawagonjetse adzachokera kotulukira dzuwa (1-7)
Isiraeli anasankhidwa kuti akhale mtumiki wa Mulungu (8-20)
Milungu ina ndi yosathandiza (21-29)
42
Mtumiki wa Mulungu komanso ntchito imene wapatsidwa (1-9)
Nyimbo yatsopano yotamanda Yehova (10-17)
Isiraeli ali ndi vuto losaona komanso losamva (18-25)
43
Yehova akusonkhanitsanso anthu ake (1-7)
Milungu ikuyesedwa (8-13)
Kumasulidwa kuchoka ku Babulo (14-21)
“Tiye tiimbane mlandu” (22-28)
44
Anthu osankhidwa a Mulungu adzadalitsidwa (1-5)
Palibe Mulungu wina kupatulapo Yehova (6-8)
Mafano opangidwa ndi munthu ndi opanda pake (9-20)
Yehova, Wowombola Isiraeli (21-23)
Yerusalemu adzamangidwanso kudzera mwa Koresi (24-28)
45
Koresi anadzozedwa kuti agonjetse Babulo (1-8)
Dongo silikuyenera kulimbana ndi Woliumba (9-13)
Anthu a mitundu ina anazindikira Isiraeli (14-17)
Mulungu ndi wodalirika polenga zinthu komanso poulula zamʼtsogolo (18-25)
46
47
48
Isiraeli anadzudzulidwa komanso kuyeretsedwa (1-11)
Yehova adzalanga Babulo (12-16a)
Zimene Mulungu amatiphunzitsa nʼzopindulitsa (16b-19)
“Tulukani mʼBabulo!” (20-22)
49
50
51
Ziyoni adzabwezeretsedwa nʼkukhala ngati munda wa Edeni (1-8)
Mawu olimbikitsa ochokera kwa amene anapanga Ziyoni yemwe ndi wamphamvu (9-16)
Kapu ya mkwiyo wa Yehova (17-23)
52
53
54
55
56
57
Wolungama komanso anthu okhulupirika awonongedwa (1, 2)
Uhule wauzimu wa Isiraeli waonekera (3-13)
Uthenga wotonthoza wopita kwa anthu onyozeka (14-21)
58
59
60
61
62
63
Yehova adzabwezera mitundu ya anthu (1-6)
Chikondi chokhulupirika cha Yehova nthawi yakale (7-14)
Pemphero losonyeza kulapa (15-19)
64
65
66
Kulambira koona komanso kwabodza (1-6)
Ziyoni ndi ana ake amuna (7-17)
Anthu adzasonkhana mu Yerusalemu kuti alambire (18-24)