Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • lfb sect. 4
  • Mawu Oyamba Gawo 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 4
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Mawu Oyamba Gawo 11
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Ankasamalira Banja Lake Komanso Anakhalabe Wokhulupirika
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Ndine Msilikali wa Khristu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Mawu Oyamba Gawo 5
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb sect. 4
Mose ndi Aisiraeli akuona Nyanja Yofiira ikugawika

Mawu Oyamba Gawo 4

Chigawochi chikufotokoza nkhani ya Yosefe, Yobu, Mose komanso Aisiraeli. Onsewa anapirira mayesero osiyanasiyana ochokera kwa Mdyerekezi. Ena mwa anthuwa anachitiridwa zinthu zopanda chilungamo, kuikidwa m’ndende ngakhalenso kuphedwa kumene. Koma Yehova anawateteza m’njira zosiyanasiyana. Ngati ndinu kholo, thandizani mwana wanu kumvetsa mmene atumiki a Yehova amenewa anavutikira koma n’kukhalabe okhulupirika.

Yehova anagwiritsa ntchito Miliri 10 pofuna kusonyeza kuti iyeyo ndi wamphamvu kwambiri kuposa milungu yonse ya ku Iguputo. Fotokozani mmene Yehova anatetezera anthu ake m’mbuyomu komanso mmene akuwatetezera masiku ano.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Yosefe anakana kuchita chiwerewere chifukwa ankakonda Yehova

  • Yobu sanalole kuti mavuto amene anakumana nawo asokoneze ubwenzi wake ndi Yehova

  • Mose sanaiwale kuti ndi mtumiki wa Mulungu kulikonse kumene anali

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani