Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • lfb sect. 11
  • Mawu Oyamba Gawo 11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 11
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Mawu Oyamba Gawo 4
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Kodi Yesu Khristu Ndi Ndani?
    Zimene Baibulo Limaphunzitsa
  • Mawu Oyamba Gawo 12
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Kodi Yesu Ndi Ndani?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb sect. 11
Yosefe akuphunzitsa Yesu ntchito ya ukalipentala, Mariya ndi azibale ake a Yesu akuonerera chapafupi

Mawu Oyamba Gawo 11

M’chigawochi muli nkhani zochokera m’Malemba a Chigiriki. Yesu anabadwira m’banja losauka lomwe linkakhala m’katauni kenakake. Iye ankagwira ntchito ya ukalipentala limodzi ndi bambo ake. Koma Yesu anapatsidwa udindo wopulumutsa anthu. Yehova anamusankha kuti akhale Mfumu ya Ufumu wakumwamba. Ngati ndinu kholo, thandizani mwana wanuyo kudziwa kuti Yehova anasankha mwanzeru banja komanso malo oti Yesu abadwire ndiponso akulire. Muthandizeni kudziwa zimene Yehova anachita poteteza Yesu kuti asaphedwe ndi Herode. M’chigawochi tiona umboni wakuti palibe chimene chingalepheretse Yehova kukwaniritsa cholinga chake. Tionanso kuti Yehova anatuma Yohane kuti akonzere Yesu njira. Pokambirana, tsindikani umboni wosonyeza kuti Yesu ankatsatira mfundo za Yehova kuyambira ali mwana ndipo ankazikonda kwambiri.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Nthawi zonse tizitsatira malangizo a Yehova

  • Yesu anali Mwana wa Mulungu wamphamvu koma analolera kudzabadwa padzikoli

  • Yohane M’batizi anathandiza anthu kukonzekera kubwera kwa Mesiya

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani